1 Timoteyo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamaso pa Mulungu, amene amathandiza kuti zinthu zonse zikhalebe zamoyo ndiponso pamaso pa Khristu Yesu, amene anapereka umboni wabwino kwambiri pamaso pa Pontiyo Pilato,+ ndikukulamula
13 Pamaso pa Mulungu, amene amathandiza kuti zinthu zonse zikhalebe zamoyo ndiponso pamaso pa Khristu Yesu, amene anapereka umboni wabwino kwambiri pamaso pa Pontiyo Pilato,+ ndikukulamula