-
1 Timoteyo 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kunena zoona, chinsinsi chopatulika chokhudza kukhala odzipereka kwa Mulungu kumeneku nʼchachikulu: ‘Iye anaonekera ngati munthu,+ anaonedwa kuti ndi wolungama pamene anali mzimu,+ anaonekera kwa angelo,+ analalikidwa kwa mitundu ya anthu,+ anthu padziko lapansi anamukhulupirira+ ndiponso analandiridwa kumwamba mu ulemerero.’
-