Luka 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atatero anayamba kuwatanthauzira zinthu zokhudza iyeyo mʼMalemba onse, kuyambira ndi Zolemba za Mose komanso zonse zimene aneneri analemba.+ Machitidwe 10:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Aneneri onse amachitira umboni za iyeyu,+ kuti aliyense womukhulupirira, machimo ake amakhululukidwa mʼdzina lake.”+
27 Atatero anayamba kuwatanthauzira zinthu zokhudza iyeyo mʼMalemba onse, kuyambira ndi Zolemba za Mose komanso zonse zimene aneneri analemba.+
43 Aneneri onse amachitira umboni za iyeyu,+ kuti aliyense womukhulupirira, machimo ake amakhululukidwa mʼdzina lake.”+