Genesis 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anapitiriza kuti: “Ine ndamva kuti ku Iguputo kuli tirigu. Pitani mukatigulire kuti tikhalebe ndi moyo, tisafe ndi njala.”+ Genesis 42:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yosefe ndi amene anali wolamulira mʼdzikomo+ ndipo ndi amene ankagulitsa tirigu kwa anthu onse ochokera kumayiko ena onse.+ Choncho abale a Yosefe anafika kwa iye ndipo anagwada nʼkumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+
2 Anapitiriza kuti: “Ine ndamva kuti ku Iguputo kuli tirigu. Pitani mukatigulire kuti tikhalebe ndi moyo, tisafe ndi njala.”+
6 Yosefe ndi amene anali wolamulira mʼdzikomo+ ndipo ndi amene ankagulitsa tirigu kwa anthu onse ochokera kumayiko ena onse.+ Choncho abale a Yosefe anafika kwa iye ndipo anagwada nʼkumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+