Ekisodo 1:7, 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aisiraeli* anaberekana ndipo anachuluka kwambiri mʼdzikomo. Iwo anapitiriza kukhala amphamvu komanso anachulukana mofulumira kwambiri, moti anadzaza mʼdzikomo.+ 8 Patapita nthawi, mfumu ina yomwe sinkamudziwa Yosefe inayamba kulamulira ku Iguputo.
7 Aisiraeli* anaberekana ndipo anachuluka kwambiri mʼdzikomo. Iwo anapitiriza kukhala amphamvu komanso anachulukana mofulumira kwambiri, moti anadzaza mʼdzikomo.+ 8 Patapita nthawi, mfumu ina yomwe sinkamudziwa Yosefe inayamba kulamulira ku Iguputo.