Ekisodo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwanayo atafika poti sangathenso kumubisa,+ anatenga kabasiketi* kagumbwa* nʼkukamata phula. Kenako anaikamo mwanayo nʼkukasiya kabasiketiko pakati pa mabango mʼmphepete mwa mtsinje wa Nailo.
3 Mwanayo atafika poti sangathenso kumubisa,+ anatenga kabasiketi* kagumbwa* nʼkukamata phula. Kenako anaikamo mwanayo nʼkukasiya kabasiketiko pakati pa mabango mʼmphepete mwa mtsinje wa Nailo.