-
Ekisodo 11:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno Yehova anachititsa kuti Aiguputo akomere mtima Aisiraeli. Komanso Mose ankalemekezedwa kwambiri mʼdziko la Iguputo, pamaso pa atumiki a Farao ndi pamaso pa Aiguputo onse.
-