Ekisodo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Yehova anamuuza Mose ali ku Midiyani kuti: “Nyamuka, bwerera ku Iguputo, chifukwa onse amene ankafuna kukupha* anafa.”+
19 Ndiyeno Yehova anamuuza Mose ali ku Midiyani kuti: “Nyamuka, bwerera ku Iguputo, chifukwa onse amene ankafuna kukupha* anafa.”+