Ekisodo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ine ndidzalola Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zodabwitsa zochuluka mʼdziko la Iguputo.+
3 Koma ine ndidzalola Farao kuti aumitse mtima wake,+ ndipo ndidzachita zizindikiro ndi zodabwitsa zochuluka mʼdziko la Iguputo.+