Machitidwe 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Saulo anavomereza zoti Sitefano aphedwe.+ Tsiku limenelo, mpingo umene unali ku Yerusalemu unayamba kuzunzidwa koopsa. Choncho ophunzira onse, kupatula atumwi okha, anabalalika nʼkupita mʼzigawo za Yudeya ndi Samariya.+ Machitidwe 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komanso pamene Sitefano, mboni yanu ankaphedwa, ine ndinali pomwepo ndipo ndinavomereza. Ndi inenso amene ndinkayangʼanira malaya akunja a anthu amene ankamuphawo.’+
8 Saulo anavomereza zoti Sitefano aphedwe.+ Tsiku limenelo, mpingo umene unali ku Yerusalemu unayamba kuzunzidwa koopsa. Choncho ophunzira onse, kupatula atumwi okha, anabalalika nʼkupita mʼzigawo za Yudeya ndi Samariya.+
20 Komanso pamene Sitefano, mboni yanu ankaphedwa, ine ndinali pomwepo ndipo ndinavomereza. Ndi inenso amene ndinkayangʼanira malaya akunja a anthu amene ankamuphawo.’+