46 ndipo anawauza kuti, “Malemba amanena kuti: Khristu adzazunzika ndipo tsiku lachitatu adzauka kwa akufa,+ 47 ndipo mʼdzina lake, uthenga woti anthu alape machimo awo+ kuti akhululukidwe udzalalikidwa kwa anthu a mitundu yonse,+ kuyambira ku Yerusalemu.+