Mateyu 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani kapena kumvetsera mawu anu, mukamatuluka mʼnyumba imeneyo kapena mumzinda umenewo muzisansa fumbi kumapazi anu.+ Luka 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani, mukamatuluka mumzinda umenewo muzisansa fumbi kumapazi anu kuti ukhale umboni wowatsutsa.”+
14 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani kapena kumvetsera mawu anu, mukamatuluka mʼnyumba imeneyo kapena mumzinda umenewo muzisansa fumbi kumapazi anu.+
5 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani, mukamatuluka mumzinda umenewo muzisansa fumbi kumapazi anu kuti ukhale umboni wowatsutsa.”+