Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 147:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Imbirani amene amaphimba mapiri ndi mitambo,

      Amene amapereka mvula padziko lapansi,+

      Amenenso amameretsa udzu+ mʼmapiri.

  • Yeremiya 5:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mumtima mwawo sanena kuti:

      “Tiyeni tsopano tiope Yehova Mulungu wathu,

      Amene amatigwetsera mvula mʼnyengo yake,

      Amatigwetsera mvula yoyamba ndi yomalizira,

      Amene amaonetsetsa kuti tikukolola pa nthawi yake.”*+

  • Mateyu 5:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 kuti musonyeze kuti ndinudi ana a Atate wanu wakumwamba.+ Chifukwa iye amawalitsira dzuwa lake anthu abwino ndi oipa omwe, ndipo amagwetsera mvula anthu olungama ndi osalungama omwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena