Machitidwe 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wa Chiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki.
16 Kenako Paulo anafika ku Debe ndiponso ku Lusitara.+ Kumeneko kunali wophunzira wina dzina lake Timoteyo,+ mwana wa mayi wa Chiyuda wokhulupirira, koma bambo ake anali Mgiriki.