2 Akorinto 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kuwonjezera pa zinthu zimenezi, palinso chinthu china chomwe panopa chimandivutitsa maganizo tsiku ndi tsiku. Ndimadera nkhawa mipingo yonse.+
28 Kuwonjezera pa zinthu zimenezi, palinso chinthu china chomwe panopa chimandivutitsa maganizo tsiku ndi tsiku. Ndimadera nkhawa mipingo yonse.+