Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 9:19, 20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Atadya chakudya anapezanso mphamvu.

      Iye anakhala ndi ophunzira ku Damasiko kwa masiku angapo.+ 20 Nthawi yomweyo anayamba kulalikira za Yesu mʼmasunagoge, kuti ameneyu ndi Mwana wa Mulungu.

  • Machitidwe 13:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako Paulo ndi anzakewo, anayamba ulendo wa panyanja kuchoka ku Pafo, ndipo anakafika ku Pega, ku Pamfuliya. Koma Yohane+ anawasiya nʼkubwerera ku Yerusalemu.+ 14 Atachoka ku Pega anakafika ku Antiokeya wa ku Pisidiya. Kumeneko analowa mʼsunagoge+ tsiku la Sabata nʼkukhala pansi.

  • Machitidwe 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Paulo ndi Baranaba ali ku Ikoniyo, analowa mʼsunagoge wa Ayuda ndipo analankhula bwino kwambiri moti Ayuda ambiri limodzi ndi Agiriki anakhala okhulupirira.

  • Machitidwe 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Paulo ankakamba nkhani mʼsunagoge+ tsiku la sabata lililonse+ ndipo ankakopa Ayuda ndi Agiriki.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena