Machitidwe 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma usiku wa tsiku lomwelo, Ambuye anaima pafupi ndi Paulo nʼkumuuza kuti: “Limba mtima.+ Chifukwa wandichitira umboni mokwanira ku Yerusalemu, ndipo ukandichitiranso umboni ku Roma.”+
11 Koma usiku wa tsiku lomwelo, Ambuye anaima pafupi ndi Paulo nʼkumuuza kuti: “Limba mtima.+ Chifukwa wandichitira umboni mokwanira ku Yerusalemu, ndipo ukandichitiranso umboni ku Roma.”+