Machitidwe 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Panali munthu wina wosula siliva dzina lake Demetiriyo. Amisiri ankapindula kwambiri chifukwa cha ntchito yake yopanga tiakachisi tasiliva ta Atemi.+
24 Panali munthu wina wosula siliva dzina lake Demetiriyo. Amisiri ankapindula kwambiri chifukwa cha ntchito yake yopanga tiakachisi tasiliva ta Atemi.+