Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 9:23, 24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndiyeno atalowa mʼnyumba ya wolamulira uja, anaona anthu akuliza zitoliro komanso gulu la anthu likulira mofuula.+ 24 Yesu anawauza kuti: “Tulukani muno, chifukwa mtsikanayu sanamwalire, koma akugona.”+ Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kumuseka monyoza.

  • Yohane 11:39, 40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Yesu anati: “Chotsani chimwalachi.” Marita, mchemwali wa womwalirayo anauza Yesu kuti: “Ambuye, pano ayenera kuti wayamba kununkha, chifukwa lero ndi tsiku la 4 chimuikireni mʼmanda.” 40 Yesu anamuuza kuti: “Kodi sindinakuuze kuti ngati ungakhulupirire udzaona ulemerero wa Mulungu?”+

  • Machitidwe 9:39, 40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Petulo atamva zimenezi, ananyamuka nʼkupita nawo limodzi. Atafika, anamutenga nʼkupita naye mʼchipinda chamʼmwamba chija. Akazi onse amasiye anabwera kwa iye akulira ndipo ankamuonetsa zovala zambiri ndiponso mikanjo imene Dorika ankasoka pamene anali nawo. 40 Petulo anauza anthu onse kuti atuluke,+ ndiyeno anagwada nʼkupemphera. Kenako anatembenuka nʼkuyangʼana mtembowo nʼkunena kuti: “Tabita, dzuka!” Ndiyeno mayiyo anatsegula maso ndipo ataona Petulo, anadzuka nʼkukhala tsonga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena