Machitidwe 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno pambuyo pa zaka zambiri, ndinabwera kudzapereka mphatso zachifundo+ kwa anthu a mtundu wanga ndiponso kudzapereka nsembe.
17 Ndiyeno pambuyo pa zaka zambiri, ndinabwera kudzapereka mphatso zachifundo+ kwa anthu a mtundu wanga ndiponso kudzapereka nsembe.