Salimo 110:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja+Mpaka nditaika adani ako kuti akhale chopondapo mapazi ako.”+ Luka 20:42, 43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Chifukwa Davideyo ananena mʼbuku la Masalimo kuti, ‘Yehova* anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja 43 mpaka nditaika adani ako kuti akhale chopondapo mapazi ako.”’+ 1 Akorinto 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chifukwa ayenera kukhala mfumu nʼkumalamulira mpaka Mulungu ataika adani onse pansi pa mapazi ake.+ Aheberi 10:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma munthu ameneyu anapereka nsembe imodzi yamachimo yothandiza mpaka kalekale, ndipo anakhala kudzanja lamanja la Mulungu.+ 13 Kuyambira nthawi imeneyo, akudikira mpaka pamene adani ake adzaikidwe kuti akhale chopondapo mapazi ake.+
110 Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja+Mpaka nditaika adani ako kuti akhale chopondapo mapazi ako.”+
42 Chifukwa Davideyo ananena mʼbuku la Masalimo kuti, ‘Yehova* anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja 43 mpaka nditaika adani ako kuti akhale chopondapo mapazi ako.”’+
25 Chifukwa ayenera kukhala mfumu nʼkumalamulira mpaka Mulungu ataika adani onse pansi pa mapazi ake.+
12 Koma munthu ameneyu anapereka nsembe imodzi yamachimo yothandiza mpaka kalekale, ndipo anakhala kudzanja lamanja la Mulungu.+ 13 Kuyambira nthawi imeneyo, akudikira mpaka pamene adani ake adzaikidwe kuti akhale chopondapo mapazi ake.+