-
Machitidwe 2:46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 Tsiku lililonse ankasonkhana mʼkachisi mogwirizana. Ankaitanirana chakudya mʼnyumba zawo ndiponso ankagawana zakudya mosangalala komanso ndi mtima wonse.
-