Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse amene amandiona amandiseka.+Iwo amandinyogodola nʼkumapukusa mitu yawo mondinyoza nʼkumati:+ Salimo 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Musalole kuti anthu amene amadana nane popanda chifukwa+ asangalale chifukwa cha mavuto anga.Musalole kuti anthu amene amadana nane popanda chifukwa andipsinyire diso mondinyoza.+ Yesaya 50:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Msana wanga ndinaupereka kwa anthu amene ankandimenyaNdipo masaya anga ndinawapereka kwa anthu amene ankandizula ndevu. Sindinabise nkhope yanga kuti asaichitire zinthu zochititsa manyazi komanso kuti asailavulire.+ Yesaya 53:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Analandira chilango kuti ife tikhale pamtendere,+Ndipo chifukwa cha mabala ake ifeyo tinachiritsidwa.+
7 Anthu onse amene amandiona amandiseka.+Iwo amandinyogodola nʼkumapukusa mitu yawo mondinyoza nʼkumati:+
19 Musalole kuti anthu amene amadana nane popanda chifukwa+ asangalale chifukwa cha mavuto anga.Musalole kuti anthu amene amadana nane popanda chifukwa andipsinyire diso mondinyoza.+
6 Msana wanga ndinaupereka kwa anthu amene ankandimenyaNdipo masaya anga ndinawapereka kwa anthu amene ankandizula ndevu. Sindinabise nkhope yanga kuti asaichitire zinthu zochititsa manyazi komanso kuti asailavulire.+
5 Koma iye anabayidwa+ chifukwa cha zolakwa zathu.+Anaphwanyidwa chifukwa cha zochimwa zathu.+ Analandira chilango kuti ife tikhale pamtendere,+Ndipo chifukwa cha mabala ake ifeyo tinachiritsidwa.+