-
Machitidwe 23:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 “Ine Kalaudiyo Lusiya, ndikulembera inu Wolemekezeka Bwanamkubwa Felike: Landirani moni!
-
-
Machitidwe 25:24, 25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ndiyeno Fesito ananena kuti: “Mfumu Agiripa ndi anthu nonse amene muli nafe pano, mwamuona munthuyu? Ayuda onse ku Yerusalemu komanso kuno, anandipempha kuti iyeyu sakuyeneranso kukhala ndi moyo ndipo analankhula zimenezi mofuula.+ 25 Koma ine ndinaona kuti sanachite chilichonse choyenera kuphedwa.+ Choncho iyeyu atapempha kuti akaonekere kwa Wolemekezeka, ndinaganiza zomutumiza.
-