Yohane 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 ndipo Yesu ankayenda mʼkachisimo mʼkhonde la zipilala la Solomo.+ Machitidwe 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndiponso zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse ankasonkhana Pakhonde la Zipilala la Solomo.+
12 Atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndiponso zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse ankasonkhana Pakhonde la Zipilala la Solomo.+