Agalatiya 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kale malemba ananeneratu kuti Mulungu adzaona anthu a mitundu ina kuti ndi olungama chifukwa cha chikhulupiriro. Choncho analengezeratu uthenga wabwino kwa Abulahamu wakuti: “Kudzera mwa iwe, mitundu yonse idzadalitsidwa.”+
8 Kale malemba ananeneratu kuti Mulungu adzaona anthu a mitundu ina kuti ndi olungama chifukwa cha chikhulupiriro. Choncho analengezeratu uthenga wabwino kwa Abulahamu wakuti: “Kudzera mwa iwe, mitundu yonse idzadalitsidwa.”+