Salimo 32:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Wosangalala ndi munthu amene zolakwa zake zakhululukidwa, amene machimo ake akhululukidwa.+ 2 Wosangalala ndi munthu amene Yehova sakumuona kuti ndi wolakwa,+Amene alibe mtima wachinyengo.
32 Wosangalala ndi munthu amene zolakwa zake zakhululukidwa, amene machimo ake akhululukidwa.+ 2 Wosangalala ndi munthu amene Yehova sakumuona kuti ndi wolakwa,+Amene alibe mtima wachinyengo.