-
Aroma 3:21, 22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Koma tsopano, zadziwika kuti munthu akhoza kukhala wolungama kwa Mulungu popanda kutsatira Chilamulo.+ Zimenezi zinatchulidwanso mʼChilamulo komanso zimene aneneri analemba.+ 22 Kuonedwa wolungama ndi Mulungu kumeneku kungatheke kwa onse amene amasonyeza kuti amakhulupirira Yesu Khristu, chifukwa palibe kusiyana.+
-