Aroma 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chilamulo chisanabwere, uchimo unalipo kale mʼdziko, koma munthu sangapezedwe ndi mlandu woti wachita tchimo ngati palibe lamulo.+
13 Chilamulo chisanabwere, uchimo unalipo kale mʼdziko, koma munthu sangapezedwe ndi mlandu woti wachita tchimo ngati palibe lamulo.+