Yoswa 21:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Palibe lonjezo* limene silinakwaniritsidwe, pa malonjezo onse abwino amene Yehova analonjeza nyumba ya Isiraeli. Onse anakwaniritsidwa.+
45 Palibe lonjezo* limene silinakwaniritsidwe, pa malonjezo onse abwino amene Yehova analonjeza nyumba ya Isiraeli. Onse anakwaniritsidwa.+