Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uchimo unalowa mʼdziko kudzera mwa munthu mmodzi ndipo uchimowo unabweretsa imfa.+ Choncho imfayo inafalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa . . .+ Aroma 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngakhale zili choncho, imfa inalamulira ngati mfumu kuyambira nthawi ya Adamu mpaka ya Mose, ngakhalenso kwa anthu amene sanachimwe ngati mmene anachimwira Adamu, yemwe ndi wofanana ndi amene ankabwera.+
12 Uchimo unalowa mʼdziko kudzera mwa munthu mmodzi ndipo uchimowo unabweretsa imfa.+ Choncho imfayo inafalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa . . .+
14 Ngakhale zili choncho, imfa inalamulira ngati mfumu kuyambira nthawi ya Adamu mpaka ya Mose, ngakhalenso kwa anthu amene sanachimwe ngati mmene anachimwira Adamu, yemwe ndi wofanana ndi amene ankabwera.+