Yohane 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wakuba amabwera ndi cholinga chofuna kudzaba, kudzapha ndi kudzawononga.+ Koma ine ndabwera kuti nkhosa zikhale ndi moyo komanso kuti zikhale nawo wochuluka.
10 Wakuba amabwera ndi cholinga chofuna kudzaba, kudzapha ndi kudzawononga.+ Koma ine ndabwera kuti nkhosa zikhale ndi moyo komanso kuti zikhale nawo wochuluka.