Agalatiya 5:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma makhalidwe amene anthu amakhala nawo mothandizidwa ndi mzimu woyera* ndi chikondi, chimwemwe, mtendere, kuleza mtima, kukoma mtima, ubwino,+ chikhulupiriro, 23 kufatsa ndi kudziletsa.+ Palibe lamulo loletsa makhalidwe amenewa.
22 Koma makhalidwe amene anthu amakhala nawo mothandizidwa ndi mzimu woyera* ndi chikondi, chimwemwe, mtendere, kuleza mtima, kukoma mtima, ubwino,+ chikhulupiriro, 23 kufatsa ndi kudziletsa.+ Palibe lamulo loletsa makhalidwe amenewa.