Mateyu 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense amene wathetsa ukwati ndi mkazi wake, osati chifukwa cha chiwerewere,* amachititsa kuti mkaziyo achite chigololo akakwatiwanso. Ndipo aliyense amene wakwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+ Mateyu 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndikukuuzani kuti aliyense amene wasiya mkazi wake nʼkukwatira wina wachita chigololo, kupatulapo ngati wamusiya chifukwa cha chiwerewere.”*+ Maliko 10:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anawauza kuti: “Aliyense amene wasiya mkazi wake nʼkukwatira wina, wachita chigololo+ ndipo walakwira mkaziyo. 12 Ndipo ngati mkazi wasiya mwamuna wake nʼkukwatiwa ndi wina, wachita chigololo.”+ Luka 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Aliyense amene wasiya mkazi wake nʼkukwatira wina, wachita chigololo ndipo aliyense amene wakwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+
32 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense amene wathetsa ukwati ndi mkazi wake, osati chifukwa cha chiwerewere,* amachititsa kuti mkaziyo achite chigololo akakwatiwanso. Ndipo aliyense amene wakwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+
9 Ine ndikukuuzani kuti aliyense amene wasiya mkazi wake nʼkukwatira wina wachita chigololo, kupatulapo ngati wamusiya chifukwa cha chiwerewere.”*+
11 Iye anawauza kuti: “Aliyense amene wasiya mkazi wake nʼkukwatira wina, wachita chigololo+ ndipo walakwira mkaziyo. 12 Ndipo ngati mkazi wasiya mwamuna wake nʼkukwatiwa ndi wina, wachita chigololo.”+
18 Aliyense amene wasiya mkazi wake nʼkukwatira wina, wachita chigololo ndipo aliyense amene wakwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+