Machitidwe 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mulungu wa makolo athu anaukitsa Yesu, amene inu munamupha pomupachika pamtengo.+ 2 Akorinto 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anafera onse kuti amene ali moyo asakhale moyo wongodzisangalatsa okha,+ koma akhale moyo wosangalatsa amene anawafera nʼkuukitsidwa.
15 Iye anafera onse kuti amene ali moyo asakhale moyo wongodzisangalatsa okha,+ koma akhale moyo wosangalatsa amene anawafera nʼkuukitsidwa.