Yakobo 1:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu aliyense amayesedwa ndi chilakolako chake chimene chimamukopa* ndi kumukola.+ 15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabereka tchimo. Ndipo tchimo likachitika, limabweretsa imfa.+
14 Koma munthu aliyense amayesedwa ndi chilakolako chake chimene chimamukopa* ndi kumukola.+ 15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabereka tchimo. Ndipo tchimo likachitika, limabweretsa imfa.+