2 Akorinto 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndipo iyeyo anationa kuti ndife oyenera kukhala atumiki a pangano latsopano,+ osati kudzera mʼmalamulo olembedwa,+ koma kudzera mu mzimu. Malamulo olembedwa amaweruza munthu kuti afe,+ koma mzimu umapatsa munthu moyo.+
6 ndipo iyeyo anationa kuti ndife oyenera kukhala atumiki a pangano latsopano,+ osati kudzera mʼmalamulo olembedwa,+ koma kudzera mu mzimu. Malamulo olembedwa amaweruza munthu kuti afe,+ koma mzimu umapatsa munthu moyo.+