1 Akorinto 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu anatiululira ifeyo zinthu zimenezi+ kudzera mwa mzimu wake,+ chifukwa mzimu umafufuza zinthu zonse, ngakhale zinthu zozama za Mulungu.+ 1 Akorinto 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ife sitinalandire mzimu wa dziko, koma mzimu wochokera kwa Mulungu,+ kuti tidziwe zinthu zimene Mulungu watipatsa mokoma mtima. 2 Akorinto 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye watidinda chidindo chake.+ Chidindo chimenechi ndi mzimu woyera+ womwe uli mʼmitima mwathu ndipo uli ngati madalitso amʼtsogolo.
10 Mulungu anatiululira ifeyo zinthu zimenezi+ kudzera mwa mzimu wake,+ chifukwa mzimu umafufuza zinthu zonse, ngakhale zinthu zozama za Mulungu.+
12 Ife sitinalandire mzimu wa dziko, koma mzimu wochokera kwa Mulungu,+ kuti tidziwe zinthu zimene Mulungu watipatsa mokoma mtima.
22 Iye watidinda chidindo chake.+ Chidindo chimenechi ndi mzimu woyera+ womwe uli mʼmitima mwathu ndipo uli ngati madalitso amʼtsogolo.