Yohane 8:31, 32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Yesu anapitiriza kuuza Ayuda amene anamukhulupirirawo kuti: “Mukapitiriza kusunga mawu anga, ndiye kuti ndinudi ophunzira anga. 32 Mudzadziwa choonadi+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+ 1 Akorinto 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Monga zilili kuti anthu onse amafa chifukwa cha Adamu,+ anthu onse adzapatsidwanso moyo kudzera mwa Khristu.+
31 Ndiyeno Yesu anapitiriza kuuza Ayuda amene anamukhulupirirawo kuti: “Mukapitiriza kusunga mawu anga, ndiye kuti ndinudi ophunzira anga. 32 Mudzadziwa choonadi+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+
22 Monga zilili kuti anthu onse amafa chifukwa cha Adamu,+ anthu onse adzapatsidwanso moyo kudzera mwa Khristu.+