Yesaya 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene amanena kuti ndine wolungama ali pafupi. Ndi ndani angandiimbe* mlandu?+ Tiyeni tikaonane pabwalo lamilandu. Kodi ndi ndani amene akufuna kundiimba mlandu? Abwere pafupi ndi ine.
8 Amene amanena kuti ndine wolungama ali pafupi. Ndi ndani angandiimbe* mlandu?+ Tiyeni tikaonane pabwalo lamilandu. Kodi ndi ndani amene akufuna kundiimba mlandu? Abwere pafupi ndi ine.