Deuteronomo 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati munthu ali ndi mwana wamwamuna wosamvera komanso wopanduka, amene samvera bambo ake kapena mayi ake,+ ndipo ayesetsa kumulangiza koma amakana kuwamvera,+ Deuteronomo 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako amuna onse a mumzinda wawo azimuponya miyala nʼkumupha. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva nʼkuchita mantha.+
18 Ngati munthu ali ndi mwana wamwamuna wosamvera komanso wopanduka, amene samvera bambo ake kapena mayi ake,+ ndipo ayesetsa kumulangiza koma amakana kuwamvera,+
21 Kenako amuna onse a mumzinda wawo azimuponya miyala nʼkumupha. Choncho muzichotsa woipayo pakati panu, ndipo Aisiraeli onse adzamva nʼkuchita mantha.+