14 Ndipo maganizo awo anachita khungu.+ Mpaka lero, nsaluyo imakhalabe yophimba pangano lakale likamawerengedwa,+ chifukwa imachotsedwa kudzera mwa Khristu basi.+ 15 Ndipotu mpaka pano, zimene Mose analemba zikamawerengedwa,+ mitima yawo imakhalabe yophimba.+