Aroma 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiye kodi zikatero Ayudafe tili pabwino kuposa ena? Ayi ndithu. Chifukwa monga tanena kale, Ayuda ndiponso Agiriki, onse amalamuliridwa ndi uchimo+
9 Ndiye kodi zikatero Ayudafe tili pabwino kuposa ena? Ayi ndithu. Chifukwa monga tanena kale, Ayuda ndiponso Agiriki, onse amalamuliridwa ndi uchimo+