1 Akorinto 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Thupi ndi limodzi, koma lili ndi ziwalo zambiri ndipo ziwalo zonse za thupi, ngakhale kuti nʼzambiri, zimapanga thupi limodzi.+ Ndi mmenenso zilili ndi Khristu.
12 Thupi ndi limodzi, koma lili ndi ziwalo zambiri ndipo ziwalo zonse za thupi, ngakhale kuti nʼzambiri, zimapanga thupi limodzi.+ Ndi mmenenso zilili ndi Khristu.