-
1 Atesalonika 5:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Tsopano tikukupemphani abale, kuti muzilemekeza anthu amene akugwira ntchito mwakhama pakati panu, amenenso amakutsogolerani mwa Ambuye komanso kukulangizani.
-