Luka 21:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho khalani maso+ ndipo muzipemphera mopembedzera nthawi zonse,+ kuti mudzathe kuthawa zinthu zonsezi zimene zikuyenera kuchitika, komanso kuti mudzathe kuima pamaso pa Mwana wa munthu.”+ 1 Atesalonika 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho tisapitirize kugona ngati mmene ena onse akuchitira,+ koma tikhalebe maso+ ndipo tikhalebe oganiza bwino.+
36 Choncho khalani maso+ ndipo muzipemphera mopembedzera nthawi zonse,+ kuti mudzathe kuthawa zinthu zonsezi zimene zikuyenera kuchitika, komanso kuti mudzathe kuima pamaso pa Mwana wa munthu.”+
6 Choncho tisapitirize kugona ngati mmene ena onse akuchitira,+ koma tikhalebe maso+ ndipo tikhalebe oganiza bwino.+