1 Akorinto 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muzitsanzira ine, ngati mmene inenso ndimatsanzirira Khristu.+ Agalatiya 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa nonsenu amene munabatizidwa ndipo ndinu ogwirizana ndi Khristu mwakhala ndi makhalidwe ngati a Khristu.+ Aefeso 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo muvale umunthu watsopano+ umene unalengedwa mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu. Mukachita zimenezi mudzatha kuchita zimene zilidi zolungama ndi zokhulupirika.
27 Chifukwa nonsenu amene munabatizidwa ndipo ndinu ogwirizana ndi Khristu mwakhala ndi makhalidwe ngati a Khristu.+
24 Ndipo muvale umunthu watsopano+ umene unalengedwa mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu. Mukachita zimenezi mudzatha kuchita zimene zilidi zolungama ndi zokhulupirika.