Machitidwe 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira+ woti iyeyu ndi amene Mulungu anamupatsa udindo woweruza anthu amoyo ndi akufa.+ 2 Akorinto 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa aliyense wa ife adzaonekera kumpando woweruzira milandu wa Khristu, kuti alandire mphoto yake mogwirizana ndi zimene anachita ali mʼthupi, kaya zabwino kapena zoipa.+
42 Ndiponso, anatilamula kuti tilalikire kwa anthu ndi kupereka umboni wokwanira+ woti iyeyu ndi amene Mulungu anamupatsa udindo woweruza anthu amoyo ndi akufa.+
10 Chifukwa aliyense wa ife adzaonekera kumpando woweruzira milandu wa Khristu, kuti alandire mphoto yake mogwirizana ndi zimene anachita ali mʼthupi, kaya zabwino kapena zoipa.+