Mateyu 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana iti timene timandikhulupirira, zingamukhalire bwino kwambiri kumumangirira chimwala cha mphero mʼkhosi mwake chimene bulu amayendetsa, nʼkumuponyera mʼnyanja yakuya.+ 1 Akorinto 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma muzisamala kuti ufulu wanu wosankhawo usakhale chopunthwitsa kwa anthu ofooka.+ 1 Akorinto 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Muzipewa kukhumudwitsa Ayuda, Agiriki ndiponso mpingo wa Mulungu.+
6 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana iti timene timandikhulupirira, zingamukhalire bwino kwambiri kumumangirira chimwala cha mphero mʼkhosi mwake chimene bulu amayendetsa, nʼkumuponyera mʼnyanja yakuya.+