-
2 Timoteyo 1:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndikuthokoza Mulungu amene ndikumuchitira utumiki wopatulika ngati mmene makolo anga akale anachitira. Ndikuuchita ndi chikumbumtima choyera ndipo sindiiwala kukutchula mʼmapemphero anga opembedzera, usana ndi usiku.
-